Machitidwe a Atumwi 7:57 - Buku Lopatulika57 Koma anafuula ndi mau aakulu, natseka m'makutu mwao, namgumukira iye ndi mtima umodzi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201457 Koma anafuula ndi mau akulu, natseka m'makutu mwao, namgumukira iye ndi mtima umodzi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa57 Koma iwo adafuula kwambiri, natseka m'makutu mwao, namgudukira onse pamodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero57 Koma iwo anatseka mʼmakutu mwawo, ndipo anafuwula kolimba, onse anathamangira kwa iye, Onani mutuwo |