Machitidwe a Atumwi 7:41 - Buku Lopatulika41 Ndipo anapanga mwanawang'ombe masiku omwewo, nabwera nayo nsembe kwa fanolo, nasekerera ndi ntchito za manja ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Ndipo anapanga mwanawang'ombe masiku omwewo, nabwera nayo nsembe kwa fanolo, nasekerera ndi ntchito za manja ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Tsono masiku amenewo iwo adapanga fano la mwanawang'ombe. Adapereka nsembe kwa fanoli, nakondwerera ntchito za manja ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Iyi ndi nthawi imene anapanga fano la mwana wangʼombe. Anapereka nsembe kwa fanoli nachita chikondwerero kulemekeza ntchito ya manja awo. Onani mutuwo |