Machitidwe a Atumwi 7:4 - Buku Lopatulika4 Pamenepo anatuluka m'dziko la Akaldeya namanga mu Harani: ndipo, kuchokera kumeneko, atamwalira atate wake, Mulungu anamsuntha alowe m'dziko lino, m'mene mukhalamo tsopano; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Pamenepo anatuluka m'dziko la Akaldeya namanga m'Harani: ndipo, kuchokera kumeneko, atamwalira atate wake, Mulungu anamsuntha alowe m'dziko lino, m'mene mukhalamo tsopano; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Tsono adatulukadi m'dziko la Akaldeya nakakhala ku Harani. Bambo wake atamwalira, Mulungu adamchotsa kumeneko, nakamufikitsa ku dziko lino kumene inu mukukhala tsopano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 “Ndipo iye anatulukadi mʼdziko la Akaldeya ndi kukakhala ku Harani. Atamwalira abambo ake, Mulungu anamuchotsa kumeneko ndi kumubweretsa mʼdziko lino limene inu mukukhalamo tsopano. Onani mutuwo |