Machitidwe a Atumwi 7:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo Yosefe anatumiza, naitana Yakobo atate wake, ndi a banja lake lonse, ndiwo anthu makumi asanu ndi awiri mphambu asanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo Yosefe anatumiza, naitana Yakobo atate wake, ndi a banja lake lonse, ndiwo anthu makumi asanu ndi awiri mphambu asanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Tsono Yosefe adaitanitsa Yakobe, bambo wake, pamodzi ndi banja lake lonse. Onse pamodzi anali anthu 75. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Izi zinachitika, Yosefe anayitanitsa abambo ake Yakobo ndi banja lonse, onse pamodzi analipo 75. Onani mutuwo |