Machitidwe a Atumwi 7:12 - Buku Lopatulika12 Koma pakumva Yakobo kuti muli tirigu mu Ejipito, anatuma makolo athu ulendo woyamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Koma pakumva Yakobo kuti muli tirigu m'Ejipito, anatuma makolo athu ulendo woyamba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Pamene Yakobe adamva kuti ku Ejipito kuli tirigu, adatumako makolo athu aja. Uwu unali ulendo wao woyamba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Pamene Yakobo anamva kuti ku Igupto kunali tirigu, iye anatuma makolo athu ulendo woyamba. Onani mutuwo |