Machitidwe a Atumwi 7:11 - Buku Lopatulika11 Koma inadza njala pa Ejipito ndi Kanani yense, ndi chisautso chachikulu; ndipo sanapeze chakudya makolo athu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Koma inadza njala pa Ejipito ndi Kanani lonse, ndi chisautso chachikulu; ndipo sanapeza chakudya makolo athu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Koma mudadzaloŵa njala m'dziko lonse la Ejipito, ndiponso m'Kanani, kotero kuti anthu adazunzika kwambiri. Makolo athu omwe sadathe kupeza chakudya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 “Kenaka munalowa njala mʼdziko la Kanaani, kotero kuti anthu anavutika kwambiri, ndipo makolo athu sanathe kupeza chakudya. Onani mutuwo |