Machitidwe a Atumwi 7:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo mkulu wa ansembe anati, Zitero izi kodi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo mkulu wa ansembe anati, Zitero izi kodi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Mkulu wa ansembe onse adafunsa Stefano kuti, “Kodi zimenezi nzoona?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Kenaka mkulu wa ansembe anafunsa Stefano kuti, “Kodi zimene akukunenerazi ndi zoona?” Onani mutuwo |