Machitidwe a Atumwi 5:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo Petro ananena naye, Undiuze, ngati munagulitsa mundawo pa mtengo wakuti. Ndipo ananena, Inde, wakuti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo Petro ananena naye, Undiuze, ngati munagulitsa mundawo pa mtengo wakuti. Ndipo ananena, Inde, wakuti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Petro adamufunsa kuti, “Tandiwuzani, kodi pogulitsa munda wanu, mtengo wake unali ndalama izi?” Maiyo adati, “Inde, mtengo wake unali womwewo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Petro anamufunsa iye kuti, “Tandiwuza, kodi izi ndi ndalama zonse zimene iwe ndi Hananiya munalandira mutagulitsa munda?” Mkaziyo anati, “Inde ndi zimenezo.” Onani mutuwo |