Machitidwe a Atumwi 5:7 - Buku Lopatulika7 Koma atapita monga maora atatu, ndipo mkazi wake, wosadziwa chidachitikacho, analowa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Koma atapita monga maora atatu, ndipo mkazi wake, wosadziwa chidachitikacho, analowa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Patapita ngati maora atatu, mkazi wake adaloŵa, osadziŵa zimene zachitika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Patapita maora atatu mkazi wake analowa, wosadziwa zimene zinachitika. Onani mutuwo |