Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 5:6 - Buku Lopatulika

6 Ndipo ananyamuka anyamata, namkulunga, namnyamula, natuluka naye, namuika.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Ndipo ananyamuka anyamata, namkulunga, namnyamula, natuluka naye, namuika.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Tsono achinyamata adabwera namkulunga m'nsalu. Adamnyamula nakamuika m'manda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Kenaka anyamata anafika, nakulunga thupi lake, ndipo anamunyamula ndi kukamuyika mʼmanda.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 5:6
5 Mawu Ofanana  

Ndipo anatenga Abisalomu namponya m'chidzenje chachikulu kunkhalangoko; naunjika pamwamba pake mulu waukulu ndithu wamiyala; ndipo Aisraele onse anathawa yense ku hema wake.


Pamenepo anatenga mtembo wa Yesu, nauzenenga ndi nsalu zabafuta pamodzi ndi zonunkhira, monga mwa maikidwe a maliro a Ayuda.


Koma atapita monga maora atatu, ndipo mkazi wake, wosadziwa chidachitikacho, analowa.


mtembo wake usakhale pamtengo usiku wonse, koma mumuike ndithu tsiku lomwelo; pakuti wopachikidwa pamtengo atembereredwa ndi Mulungu; kuti mungadetse dziko lanu limene Yehova Mulungu wanu akupatsani likhale cholowa chanu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa