Machitidwe a Atumwi 3:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo anazunzuka, naimirira, nayenda; ndipo analowa pamodzi nao mu Kachisi, nayenda, nalumpha, nayamika Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo anazunzuka, naimirira, nayenda; ndipo analowa pamodzi nao m'Kachisi, nayenda, nalumpha, nayamika Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Adalumpha, naimirira, nayamba kuyenda, ndipo adaloŵa nao m'Nyumba ya Mulungu akuyenda ndi kulumpha ndi kutamanda Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Iye analumpha ndi kuyamba kuyenda. Kenaka analowa nawo pamodzi mʼbwalo la Nyumba ya Mulungu, akuyenda ndi kulumpha ndiponso kuyamika Mulungu. Onani mutuwo |