Machitidwe a Atumwi 3:10 - Buku Lopatulika10 namzindikira iye, kuti ndiye amene anakhala pa Chipata Chokongola cha Kachisi: ndipo anadzazidwa ndi kudabwa ndi kuzizwa pa ichi chidamgwera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 namzindikira iye, kuti ndiye amene anakhala pa Khomo Lokongola la Kachisi: ndipo anadzazidwa ndi kudabwa ndi kuzizwa pa ichi chidamgwera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Adamzindikira kuti ndi yemwe uja amene ankakhala pa Khomo Lokongola la Nyumba ya Mulungu. Ndipo adazizwa ndithu ndi kudabwa ndi zimene zidamchitikira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 anamuzindikira kuti ndi yemwe uja ankakhala pa khomo la Nyumbayo lotchedwa Khomo Lokongola, ndipo anazizwa ndi kudabwa ndi zimene zinamuchitikira. Onani mutuwo |