Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 26:8 - Buku Lopatulika

8 Muchiyesa chinthu chosakhulupirika, chakuti Mulungu aukitsa akufa?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Muchiyesa chinthu chosakhulupirika, chakuti Mulungu aukitsa akufa?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Bwanji ena mwa inu Ayuda mumayesa kuti nkosatheka kukhulupirira kuti Mulungu nkuukitsa anthu kwa akufa?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Nʼchifukwa chiyani ena a inu mukuganiza kuti nʼkosatheka kuti Mulungu aukitse akufa?

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 26:8
14 Mawu Ofanana  

Kodi chilipo chinthu chomkanika Yehova? Pa nthawi yoikidwa ndidzabwera kwa iwe, pakufika nyengo yake, ndipo Sara adzakhala ndi mwana wamwamuna.


Chifukwa palibe mau amodzi akuchokera kwa Mulungu adzakhala opanda mphamvu.


Koma Iye anati, Zinthu zosatheka ndi anthu zitheka ndi Mulungu.


Koma pozindikira Paulo kuti ena ndi Asaduki, ndi ena Afarisi, anafuula m'bwalomo, Amuna, abale, ine ndine Mfarisi, mwana wa Afarisi: andinenera mlandu wa chiyembekezo ndi kuuka kwa akufa.


koma anali nao mafunso ena otsutsana naye a chipembedzero cha iwo okha, ndi mafunso a wina Yesu, amene adafa, amene Paulo anati kuti ali ndi moyo.


ovutika mtima chifukwa anaphunzitsa anthuwo, nalalikira mwa Yesu kuuka kwa akufa.


Ukani molungama, ndipo musachimwe; pakuti ena alibe chidziwitso cha Mulungu. Ndilankhula kunyaza inu.


amene adzasanduliza thupi lathu lopepulidwa, lifanane nalo thupi lake la ulemerero, monga mwa machitidwe amene akhoza kudzigonjetsera nao zinthu zonse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa