Machitidwe a Atumwi 22:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo pakumva kuti analankhula nao m'chinenedwe cha Chihebri, anaposa kukhala chete; ndipo anati, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo pakumva kuti analankhula nao m'chinenedwe cha Chihebri, anaposa kukhala chete; ndipo anati: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Pamene iwo adamumva akulankhula nawo pa Chiyuda, adakhala chete kopambana. Tsono Paulo anati, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Atamva iye akuyankhula Chihebri, anakhala chete. Kenaka Paulo anati, Onani mutuwo |