Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 2:8 - Buku Lopatulika

8 Ndipo nanga ife timva bwanji, yense m'chilankhulidwe chathu chimene tinabadwa nacho?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndipo nanga ife timva bwanji, yense m'chilankhulidwe chathu chimene tinabadwa nacho?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Nanga bwanji aliyense mwa ife akuŵamva akulankhula chilankhulo chakwao?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Nanga bwanji aliyense wa ife akuwamva iwo mu chinenero cha kwawo?

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 2:8
5 Mawu Ofanana  

Kudziwitsa ana a anthu zamphamvu zake, ndi ulemerero waukulu wa ufumu wake.


Ndipo atate wake Zekariya anadzazidwa ndi Mzimu Woyera, nanenera za Mulungu, nati,


Ndipo anadabwa onse, nazizwa, nanena, Taonani, awa onse alankhulawa sali Agalileya kodi?


Aparti ndi Amedi, ndi Aelamu, ndi iwo akukhala mu Mesopotamiya, mu Yudeya, ndiponso mu Kapadokiya, mu Ponto, ndi mu Asiya;


Ndipotu Mulungu anaika ena mu Mpingo, poyamba atumwi, achiwiri aneneri, achitatu aphunzitsi, pamenepo zozizwa, pomwepo mphatso za machiritso, mathandizo, maweruziro, malilime a mitundumitundu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa