Machitidwe a Atumwi 2:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo anadabwa onse, nathedwa nzeru, nanena wina ndi mnzake, Kodi ichi nchiyani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo anadabwa onse, nathedwa nzeru, nanena wina ndi mnzake, Kodi ichi nchiyani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Onse adazizwa ndi kuthedwa nzeru, ndipo adayamba kufunsana kuti, “Kodi chimenechi nchiyani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Modabwa ndi mothedwa nzeru anafunsana wina ndi mnzake kuti, “Zimenezi zikutanthauzanji?” Onani mutuwo |