Machitidwe a Atumwi 17:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo pamene analandira chikole kwa Yasoni ndi enawo, anawamasula. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo pamene analandira chikole kwa Yasoni ndi enawo, anawamasula. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Koma Yasoni ndi anzake aja atalipira mlanduwo, akuluwo adaŵamasula. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Iwo analipiritsa Yasoni ndi anzakewo ndipo anawamasula. Onani mutuwo |