Machitidwe a Atumwi 17:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo anavuta anthu, ndi akulu a mzinda, pamene anamva zimenezi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo anavuta anthu, ndi akulu a mudzi, pamene anamva zimenezi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Mau ameneŵa adautsa mitima ya anthuwo ndi ya akulu amumzinda aja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Atamva zimenezi, gulu la anthu ndi akulu a mzinda anavutika mu mtima. Onani mutuwo |