Machitidwe a Atumwi 17:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo ena a iwo anakopedwa, nadziphatika kwa Paulo ndi Silasi; ndi Agriki akupembedza aunyinji ndithu, ndi akazi aakulu osati owerengeka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo ena a iwo anakopedwa, nadziphatika kwa Paulo ndi Silasi; ndi Agriki akupembedza aunyinji ndithu, ndi akazi akulu osati owerengeka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Tsono ena mwa iwo adakopeka, natsata Paulo ndi Silasi. Agriki ambirimbiri opembedza Mulungu adateronso, pamodzi ndi akazi ambiri apamwamba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ena mwa Ayuda anakopeka mtima ndipo anatsatira Paulo ndi Sila, monganso linachitira gulu lalikulu la Agriki woopa Mulungu, pamodzi ndi amayi odziwika ambiri. Onani mutuwo |