Machitidwe a Atumwi 13:9 - Buku Lopatulika9 Koma Saulo, ndiye Paulo, wodzazidwa ndi Mzimu Woyera, anampenyetsetsa iye, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Koma Saulo, ndiye Paulo, wodzazidwa ndi Mzimu Woyera, anampenyetsetsa iye, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Koma Saulo, amene ankatchedwanso Paulo, atadzazidwa ndi Mzimu Woyera, adampenyetsetsa Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Koma Saulo, amenenso amatchedwa Paulo, wodzazidwa ndi Mzimu Woyera anamuyangʼanitsitsa Elima ndipo anati, Onani mutuwo |