Machitidwe a Atumwi 11:4 - Buku Lopatulika4 Koma Petro anayamba kuwafotokozera chilongosolere, nanena, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Koma Petro anayamba kuwafotokozera chilongosolere, nanena, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Apo Petro adayamba kuŵafotokozera mwatsatanetsatane zimene zidachitika. Adati, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Koma Petro anayamba kuwafotokozera zonse mwatsatanetsatane momwe zinachitikira kuti, Onani mutuwo |