Machitidwe a Atumwi 11:3 - Buku Lopatulika3 nanena kuti, Munalowa kwa anthu osadulidwa, ndi kudya nao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 nanena kuti, Munalowa kwa anthu osadulidwa, ndi kudya nao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Iwo adati, “Inu mudaloŵa m'nyumba ya anthu osaumbalidwa, nkudya nawo pamodzi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 ndipo anati, “Iwe unalowa mʼnyumba ya anthu osachita mdulidwe ndi kudya nawo.” Onani mutuwo |