Machitidwe a Atumwi 1:12 - Buku Lopatulika12 Pamenepo anabwera ku Yerusalemu kuchokera kuphiri lonenedwa la Azitona, limene liyandikana ndi Yerusalemu, loyendako tsiku la Sabata. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Pamenepo anabwera ku Yerusalemu kuchokera kuphiri lonenedwa la Azitona, limene liyandikana ndi Yerusalemu, loyendako tsiku la Sabata. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Tsono atumwi aja adabwerera ku Yerusalemu kuchokera ku Phiri la Olivi. Mtunda wake kuchokera ku Yerusalemu ngwosakwanira ngakhale mtunda umodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Pamenepo atumwi anabwerera ku Yerusalemu kuchokera ku phiri la Olivi, mtunda wosakwana kilomita kuchokera mu mzindamo. Onani mutuwo |