Luka 9:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo Herode anati, Yohane ndinamdula mutu ine; koma uyu ndani ndikumva zotere za iye? Ndipo anafunafuna kumuona Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo Herode anati, Yohane ndinamdula mutu ine; koma uyu ndani ndikumva zotere za iye? Ndipo anafunafuna kumuona Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Herode adati, “Yohane ndiye paja ndidamdula pa khosi. Nanga uyunso ndani amene ndikumva zake zotereyu?” Choncho ankafunitsitsa kuti amuwone Yesuyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Koma Herode anati, “Ine ndinamudula mutu Yohane. Nanga uyu ndani amene ndikumva zinthu zotere za Iye?” Ndipo iye anayesetsa kuti amuone Iye. Onani mutuwo |