Luka 9:8 - Buku Lopatulika8 koma ena, kuti Eliya anaoneka; ndipo ena, kuti mneneri wina wa akale aja anauka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 koma ena, kuti Eliya anaoneka; ndipo ena, kuti mneneri wina wa akale aja anauka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Koma ena ankanena kuti, “Iyai, ameneyu ndi Eliya, waonekanso.” Enanso ankati, “Iyai, koma ndi mmodzi mwa aneneri akale aja, wauka kwa akufa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 ena amati Eliya waonekera, ndipo ena anatinso mmodzi wa aneneri akalekale waukanso. Onani mutuwo |