Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 9:57 - Buku Lopatulika

57 Ndipo m'mene iwo analikuyenda m'njira, munthu anati kwa Iye, Ine ndidzakutsatani kumene kulikonse mukapitako.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

57 Ndipo m'mene iwo analikuyenda m'njira, munthu anati kwa Iye, Ine ndidzakutsatani kumene kulikonse mukapitako.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

57 Pamene iwo anali panjira, munthu wina adauza Yesu kuti, “Ndizikutsatani kulikonse kumene muzipita.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

57 Pamene iwo ankayenda mu msewu, munthu wina anati kwa Iye, “Inu ndikutsatirani kulikonse kumene mudzapita.”

Onani mutuwo Koperani




Luka 9:57
6 Mawu Ofanana  

Ndipo anthu onse anavomera pamodzi, nati, Zonse adazilankhula Yehova tidzazichita. Ndipo Mose anabwera nao mau a anthu kwa Yehova.


Ndipo panali, pamene anayamba kukwanira masiku akuti alandiridwe Iye kumwamba, Yesu anatsimikiza kuloza nkhope yake kunka ku Yerusalemu,


Ndipo anapita kumudzi kwina.


Petro ananena ndi Iye, Ambuye, sindingathe kukutsatani Inu tsopano chifukwa ninji? Ndidzataya moyo wanga chifukwa cha Inu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa