Luka 9:53 - Buku Lopatulika53 Ndipo iwo sanamlandire Iye, chifukwa nkhope yake inali yoloza kunka ku Yerusalemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201453 Ndipo iwo sanamlandire Iye, chifukwa nkhope yake inali yoloza kunka ku Yerusalemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa53 Koma anthu am'mudzimo sadafune kumlandira, chifukwa Iye ankapita ku Yerusalemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero53 koma anthu kumeneko sanamulandire chifukwa Iye ankapita ku Yerusalemu. Onani mutuwo |