Luka 9:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo onse amene sakakulandireni inu, m'mene mutuluka m'mudzi womwewo, sansani fumbi la pa mapazi anu, likhale mboni ya paiwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo onse amene sakakulandireni inu, m'mene mutuluka m'mudzi womwewo, sansani fumbi la pa mapazi anu, likhale mboni ya paiwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Ngati kumudzi kwina anthu sakulandirani, pochoka kumeneko musanse fumbi la kumapazi kwanu. Limeneli likhale chenjezo kwa iwowo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Ngati anthu sakulandirani, sasani fumbi la kumapazi anu pomwe mukuchoka mu mzinda wawo ngati umboni owatsutsa.” Onani mutuwo |