Luka 9:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo m'nyumba iliyonse mukalowemo, khalani komweko, ndipo muzikachokera kumeneko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo m'nyumba iliyonse mukalowemo, khalani komweko, ndipo muzikachokera kumeneko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ndipo mukafikira kunyumba kwina, mukhale nao kumeneko mpaka itakwana nthaŵi yoti muchoke kumudziko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Nyumba iliyonse imene mulowa, mukhale momwemo kufikira mutachoka mu mzindawo. Onani mutuwo |