Luka 9:34 - Buku Lopatulika34 Ndipo akadalankhula izi, unadza mtambo, nuwaphimba iwo; ndipo anaopa pakulowa iwo mumtambo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Ndipo akadalankhula izi, unadza mtambo, nuwaphimba iwo; ndipo anaopa pakulowa iwo mumtambo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Akulankhula choncho, padafika mtambo nuŵaphimba, ndipo ophunzirawo adagwidwa ndi mantha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Pamene Iye ankayankhula, mtambo unaonekera ndi kuwaphimba iwo, ndipo anachita mantha pamene mtambowo unawakuta. Onani mutuwo |