Luka 9:35 - Buku Lopatulika35 Ndipo munatuluka mau mumtambo, nanena, Uyu ndiye Mwana wanga, wosankhidwayo; mverani Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Ndipo munatuluka mau mumtambo, nanena, Uyu ndiye Mwana wanga, wosankhidwayo; mverani Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Mumtambomo mudamveka mau akuti, “Uyu ndiye Mwana wanga amene ndidamsankha, muzimumvera.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Mawu anachokera mu mtambomo nati, “Uyu ndi Mwana wanga amene ndamusankha; mumvereni Iye.” Onani mutuwo |