Luka 9:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo anatero, nawakhalitsa pansi onsewo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo anatero, nawakhalitsa pansi onsewo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Ophunzira aja adaŵakhalitsadi anthu onse aja pansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Ophunzira ake anachita zomwezo ndipo aliyense anakhala pansi. Onani mutuwo |