Luka 8:56 - Buku Lopatulika56 Ndipo atate wake ndi amake anadabwa; ndipo analamulira iwo asauze munthu aliyense chimene chinachitika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201456 Ndipo atate wake ndi amake anadabwa; ndipo analamulira iwo asauze munthu aliyense chimene chinachitika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa56 Makolo ake aja adazizwa kwambiri, koma Yesu adaŵalamula kuti asauze wina aliyense zimene zidaachitikazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero56 Makolo ake anadabwa, koma Iye anawalamulira kuti asawuze wina aliyense zimene zinachitikazo. Onani mutuwo |