Luka 8:52 - Buku Lopatulika52 Ndipo anthu onse analikumlira iye ndi kudziguguda pachifuwa. Koma Iye anati, Musalire; pakuti iye sanafe, koma wagona tulo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201452 Ndipo anthu onse analikumlirira iye ndi kudziguguda pachifuwa. Koma Iye anati, Musalire; pakuti iye sanafe, koma wagona tulo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa52 Anthu onse ankalira ndi kubuma. Koma Yesu adati, “Musalire, mwanayutu sadamwalire ai, ali m'tulo chabe.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero52 Pa nthawiyi nʼkuti anthu onse akubuma ndi kumulirira iye. Yesu anati, “Lekani kulira, sanafe koma wagona tulo.” Onani mutuwo |