Luka 8:40 - Buku Lopatulika40 Ndipo pakubwera Yesu, khamu la anthu linamlandira Iye; pakuti onse analikumlindira Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Ndipo pakubwera Yesu, khamu la anthu linamlandira Iye; pakuti onse analikumlindira Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Pamene Yesu adafikanso ku tsidya, chinamtindi cha anthu chidamchingamira, popeza kuti onse ankamudikira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 Yesu atabwerera, gulu lalikulu la anthu linamulandira, chifukwa onse ankamuyembekezera. Onani mutuwo |