Luka 8:34 - Buku Lopatulika34 Ndipo akuwetawo m'mene anaona chimene chinachitika, anathawa, nauza okhala mumzinda ndi kuminda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Ndipo akuwetawo m'mene anaona chimene chinachitika, anathawa, nauza akumudzi ndi kumilaga yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Oŵeta nkhumbazo ataona zimenezi, adathaŵa, nakauza anthu ku mzinda ndi ku midzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Oweta nkhumbazo ataona zimene zinachitikazo, anathamanga ndi kukanena izi mu mzinda ndi ku madera a ku midzi. Onani mutuwo |