Luka 7:26 - Buku Lopatulika26 Koma munatuluka kukaona chiyani? Mneneri kodi? Etu, ndinena kwa inu, ndipo wakuposa mneneri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Koma munatuluka kukaona chiyani? Mneneri kodi? Etu, ndinena kwa inu, ndipo wakuposa mneneri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Tanenanitu, mudaati mukaona chiyani? Mneneri kodi? Zoonadi, ndipo ndikunenetsa kuti mudakaona woposa mneneri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Koma inu munkapita kukaona chiyani? Mneneri? Inde, Ine ndikukuwuzani, woposa mneneri. Onani mutuwo |