Luka 7:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo mbiri yake imeneyo inabuka ku Yudeya yense, ndi ku dziko lonse loyandikira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo mbiri yake imeneyo inabuka ku Yudeya lonse, ndi ku dziko lonse loyandikira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Mbiri ya Yesuyi idawanda m'dziko lonse la Yudeya, ndi ku madera onse ozungulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Mbiriyi inafalikira ku Yudeya konse ndi ku madera ozungulira. Onani mutuwo |