Luka 7:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo wakufayo anakhala tsonga, nayamba kulankhula. Ndipo anampereka kwa amake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo wakufayo anakhala tsonga, nayamba kulankhula. Ndipo anampereka kwa amake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Pamenepo wakufayo adakhala tsonga nayamba kulankhula, Yesu nkumupereka kwa mai wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Wakufayo anakhala tsonga ndi kuyamba kuyankhula, ndipo Yesu anamupereka mnyamatayo kwa amayi ake. Onani mutuwo |