Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 7:11 - Buku Lopatulika

11 Ndipo kunali, katapita kamphindi, Iye anapita kumzinda, dzina lake Naini; ndipo ophunzira ake ndi mpingo waukulu wa anthu anapita naye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndipo kunali, katapita kamphindi, Iye anapita kumudzi, dzina lake Naini; ndipo ophunzira ake ndi mpingo waukulu wa anthu anapita naye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Pambuyo pake Yesu adapita ku mudzi wina, dzina lake Naini. Ophunzira ake pamodzi ndi anthu ena ambirimbiri adatsagana naye.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Zitangotha izi, Yesu anapita ku mudzi wa Naini ndipo ophunzira ake ndi gulu lalikulu la anthu linapita naye pamodzi.

Onani mutuwo Koperani




Luka 7:11
3 Mawu Ofanana  

Ndipo pakubwera kunyumba otumidwawo, anapeza kapoloyo wachira ndithu.


Ndipo pamene anayandikira kuchipata cha mzindawo, onani, anthu analikunyamula munthu wakufa, mwana wamwamuna mmodzi yekha, amake ndiye mkazi wamasiye; ndipo anthu ambiri amumzinda anali pamodzi naye.


za Yesu wa ku Nazarete, kuti Mulungu anamdzoza Iye ndi Mzimu Woyera ndi mphamvu; amene anapitapita nachita zabwino, nachiritsa onse osautsidwa ndi mdierekezi, pakuti Mulungu anali pamodzi ndi Iye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa