Luka 6:44 - Buku Lopatulika44 Pakuti mtengo uliwonse uzindikirika ndi chipatso chake. Pakuti anthu samatchera nkhuyu paminga, kapena pamtungwi samatchera mphesa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 Pakuti mtengo uliwonse uzindikirika ndi chipatso chake. Pakuti anthu samatchera nkhuyu paminga, kapena pamtungwi samatchera mphesa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 Mtengo uliwonse umadziŵika ndi zipatso zake. Sathyola nkhuyu pa minga, kapenanso mphesa pa mtula. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 Mtengo uliwonse umadziwika ndi chipatso chake. Anthu sathyola nkhuyu pa mtengo waminga, kapena mphesa pa nthungwi. Onani mutuwo |