Luka 6:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo Yesu anayankha nati kwa iwo, Kodi simunawerenganso ngakhale chimene anachita Davide, pamene paja anamva njala, iye ndi iwo anali naye pamodzi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo Yesu anayankha nati kwa iwo, Kodi simunawerenganso ngakhale chimene anachita Davide, pamene paja anamva njala, iye ndi iwo anali naye pamodzi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Yesu adati, “Kani simudaŵerenge zimene adaachita Davide, pamene iye ndi anzake adaazingwa nayo njala? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Yesu anawayankha iwo kuti, “Kodi simunawerenge zimene Davide anachita pamene iye ndi anzake anali ndi njala? Onani mutuwo |