Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 6:18 - Buku Lopatulika

18 ndipo ovutidwa ndi mizimu yonyansa anachiritsidwa,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 ndipo ovutidwa ndi mizimu yonyansa anachiritsidwa,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Iwo adabwera kudzamva mau ake, ndiponso kuti Iye aŵachiritse. Anthu amene ankasautsidwa ndi mizimu yoipa, amenewonso Iye ankaŵachiritsa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Iwo anabwera kudzamvetsera ndi kuchiritsidwa ku matenda awo. Osautsidwa ndi mizimu yoyipa anachiritsidwa,

Onani mutuwo Koperani




Luka 6:18
5 Mawu Ofanana  

Ndipo onani, mkazi wa ku Kanani anatuluka m'malire, nafuula, nati, Mundichitire ine chifundo Ambuye, mwana wa Davide; mwana wanga wamkazi wagwidwa koopsa ndi chiwanda.


Ambuye, chitirani mwana wanga chifundo; chifukwa adwala khunyu, kuzunzika koipa: pakuti amagwa kawirikawiri pamoto, ndi kawirikawiri m'madzi.


Ndipo Iye anatsika nao, naima pachidikha, ndi khamu lalikulu la ophunzira ake, ndi unyinji waukulu wa anthu a ku Yudeya yense ndi Yerusalemu, ndi a ku mbali ya nyanja ya ku Tiro ndi Sidoni, amene anadza kudzamva Iye ndi kudzachiritsidwa nthenda zao;


ndi khamu lonse lija linafuna kumkhudza Iye; chifukwa munatuluka mphamvu mwa Iye, nkuchiritsa onsewa.


Komanso unasonkhana pamodzi unyinji wa anthu ochokera kumidzi yozungulira Yerusalemu, alikutenga odwala, ndi ovutika ndi mizimu yonyansa; ndipo anachiritsidwa onsewa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa