Luka 5:9 - Buku Lopatulika9 Pakuti chizizwo chidagwira iye, ndi onse amene anali naye, pa kusodzako kwa nsomba zimene anazikola; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Pakuti chizizwo chidagwira iye, ndi onse amene anali naye, pa kusodzako kwa nsomba zimene anazikola; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Adaatero popeza kuti iye, pamodzi ndi onse amene anali naye, adaazizwa nako kuchuluka kwa nsomba zimene adaaphazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Iye ndi anzake onse anadabwa ndi nsomba zimene anagwira, Onani mutuwo |