Luka 5:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo Iye, pakuona chikhulupiriro chao, anati, Munthu iwe, machimo ako akhululukidwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo Iye, pakuona chikhulupiriro chao, anati, Munthu iwe, machimo ako akhululukidwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Poona chikhulupiriro chaocho, Yesu adati, “Mbale wanga, machimo ako akhululukidwa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Yesu ataona chikhulupiriro chawo, anati, “Mnzanga, machimo ako akhululukidwa.” Onani mutuwo |