Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 5:16 - Buku Lopatulika

16 Koma Iye anazemba, nanka m'mapululu, nakapemphera.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Koma Iye anazemba, nanka m'mapululu, nakapemphera.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Koma Iye adapita kumalo kosapitapita anthu, namakapemphera kumeneko.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Koma Yesu nthawi zambiri ankachoka kupita ku malo a yekha kukapemphera.

Onani mutuwo Koperani




Luka 5:16
8 Mawu Ofanana  

Ndipo pamene Iye anawauza makamuwo, anakwera m'phiri pa yekha, kukapemphera: ndipo pamene panali madzulo, Iye anakhala kumeneko yekha.


Ndipo atalawirana nao, anachoka Iye, nalowa m'phiri kukapemphera.


Pamene anthu onse anabatizidwa, Yesu nayenso anabatizidwa. Iye anali kupemphera, ndipo kuthambo kunatseguka,


Ndipo kunali masiku awa, Iye anatuluka nanka kuphiri kukapemphera; nachezera usiku wonse m'kupemphera kwa Mulungu.


Ndipo pamene padatha ngati masiku asanu ndi atatu atanena mau amenewa, Iye anatenga Petro ndi Yohane ndi Yakobo apite naye, nakwera m'phiri kukapemphera.


Ndipo m'kupemphera kwake, maonekedwe a nkhope yake anasandulika, ndi chovala chake chinayera ndi kunyezimira.


Pamenepo Yesu, pozindikira kuti alikufuna kudza kudzamgwira Iye, kuti amlonge ufumu, anachokanso kunka kuphiri pa yekha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa