Luka 4:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo Yesu anayankha, nati kwa iye, Kwalembedwa, kuti, Ambuye Mulungu wako uzimgwadira, ndipo Iye yekhayekha uzimtumikira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo Yesu anayankha, nati kwa iye, Kwalembedwa, kuti, Ambuye Mulungu wako uzimgwadira, ndipo Iye yekhayekha uzimtumikira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Apo Yesu adati, “Malembo akuti, ‘Uzipembedza Ambuye Mulungu wako, ndipo uziŵatumikira Iwo okha.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Yesu anayankha kuti, “Zalembedwa: ‘Pembedza Yehova Mulungu wako ndi kumutumikira Iye yekha.’ ” Onani mutuwo |