Luka 4:39 - Buku Lopatulika39 Ndipo Iye anaimirira, naweramira pa iye, nadzudzula nthendayo; ndipo inamleka iye: ndipo anauka msangatu, nawatumikira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Ndipo Iye anaimirira, naweramira pa iye, nadzudzula nthendayo; ndipo inamleka iye: ndipo anauka msangatu, nawatumikira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Yesu adaŵeramira pa iye, nazazira malungowo, ndipo malungo aja adatha. Pomwepo amai aja adadzuka nayamba kukonzera anthu chakudya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Ndipo anawerama nadzudzula malungowo ndipo anamusiya. Anadzuka nthawi yomweyo nayamba kuwatumikira. Onani mutuwo |