Luka 4:26 - Buku Lopatulika26 ndipo Eliya sanatumidwe kwa mmodzi wa iwo, koma ku Sarepta wa ku Sidoni, kwa mkazi wamasiye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 ndipo Eliya sanatumidwa kwa mmodzi wa iwo, koma ku Sarepta wa ku Sidoni, kwa mkazi wamasiye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Eliya sadatumidwe ndi kwa mmodzi yemwetu mwa iwo aja, koma adatumidwa kwa mai wamasiye wa ku mudzi wa Sarepta, m'dziko la Sidoni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Komabe Eliya sanatumidwe kwa mmodzi mwa iwo, koma kwa mkazi wamasiye wa ku Zerefati ku chigawo cha Sidoni. Onani mutuwo |