Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 4:24 - Buku Lopatulika

24 Ndipo Iye anati, Indetu, ndinena kwa inu, kuti, Palibe mneneri alandirika kudziko la kwao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 Ndipo Iye anati, Indetu, ndinena kwa inu, kuti, Palibe mneneri alandirika kudziko la kwao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 Adaŵauzanso kuti, “Ndithu ndikunenetsa kuti palibe mneneri amene amalandiridwa bwino kumudzi kwao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Iye anapitiriza kuti, “Zoonadi, ndikukuwuzani kuti palibe mneneri amene amavomerezedwa ku mudzi kwawo.

Onani mutuwo Koperani




Luka 4:24
6 Mawu Ofanana  

Ndipo iwo anakhumudwa chifukwa cha Iye. Koma Yesu anati kwa iwo, Mneneri sakhala wopanda ulemu koma kudziko la kwao ndiko, ndi kubanja kwake.


Ndipo ambiri oposa anakhulupirira chifukwa cha mau ake;


Pakuti Yesu mwini anachita umboni kuti, Mneneri alibe ulemu m'dziko la kwao.


Ine ndine munthu Myuda, wobadwa mu Tariso wa Silisiya, koma ndaleredwa m'mzinda muno, pa mapazi a Gamaliele, wolangizidwa monga mwa chitsatidwe chenicheni cha chilamulo cha makolo athu, ndipo ndinali wachangu, cholinga kwa Mulungu, monga muli inu nonse lero;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa